TIZICHITENGA CHOONADI NGATI NYAMA

Mateyu 28:18, 19

Wanthabwala wina anati: ana akadya chankhuli amasunga kachidutsa kena kuti akawaonetse anzake nkuwagawira aliyese kapisi kakang'ono. Amafuna kuti anzaowo alaweko zabwino zomwe iwo ali nazo. Koma anawa akadya zamasamba samatero ayi.

Mipingo (zipembezo) zonse padzikoli, tingati zikudya zamasamba chifukwa sizimafuna kugawa zomwe zimaphunzitsa, koma ife (Yesaya 43:10) timagawa kwa anthu uthenga wabwino (Mateyo 24:14) omwe uli ngati chidutswa cha nyama. (Mac. 1:8)

Zatsopano

Kodi kutchova juga ndi tchimo?

Zomwe ndinapindula pa nkhani yoti:


Pewani mzimu wa dziko

  • Chifukwa chake tiyenera kuupewa
  • Tingaupewe bwanji
  • Zomwe tingachite kuti mzimu wa Yehova udzititsogolera

  • Chida chilichonse chimene chidzapangidwe kuti chikuvulaze sichizapambana

  • Zida za Satana
  • Umboni wa kulephera kwa zidazo
  • Chifukwa chake zidazi zimalephera
  • Tingalimbitse bwanji chikhulupiliro chathu?

  • Mdzikoli sitingatulukemo ndi kanthu


    Tipireke mpaka mapeto

  • Nthawi yomwe timafunika kupilira
  • Zomwe tiyenera kuchita
  • Ubwenzi wa Mulungu ndimnasi

  • Zomwe zimalimbikitsa ubale
  • Zitsanzo za omwe anasonyeza chikondi
  • Zomwe tikuphunzirapo
  • Zitsanzo

  • Kuchitenga Choonadi ngati nyama
  • Primary Site All in one History Bengo Lessons