Website ino siikuphwanya mfundo zokhuza malamulo pa JW.ORG mabuku ena omwe anapangidwa upload pano ndidzawachotsa ndikadzakhala ndi offline drive koma zonse zomwe zili pano ndi za persnal use. Monga tsamba loyamba lafotokozera, pa website ino pali zomwe ndimapindula ku misonkhano. kale ndinkazisunga mmakope koma zinayamba kuwonongeka moti nosi za msonkhano wa 2017 ndimaziona movutukira pozikopera chifukwa zinaonongedwa ndi tizilombo.
Ndie malo otetezeka omwe ndinaona kuti ndingasungepo zinthu zanga ndi amenewa.