Zitsanzo mu nkhani za ku misonkhano

TIZICHITENGA CHOONADI NGATI NYAMA

Mateyu 28:18, 19

Wanthabwala wina anati: ana akadya chankhuli amasunga kachidutsa kena kuti akawaonetse anzake nkuwagawira aliyese kapisi kakang'ono. Amafuna kuti anzaowo alaweko zabwino zomwe iwo ali nazo. Koma anawa akadya zamasamba samatero ayi.

Mipingo (zipembezo) zonse padzikoli, tingati zikudya zamasamba chifukwa sizimafuna kugawa zomwe zimaphunzitsa, koma ife (Yesaya 43:10) timagawa kwa anthu uthenga wabwino (Mateyo 24:14) omwe uli ngati chidutswa cha nyama. (Mac. 1:8)

Primary Site All in one History Bengo Lessons